Mnyamata wina wa kabadza adalirira cha kwao. Mwa ntchito yake cha - TopicsExpress



          

Mnyamata wina wa kabadza adalirira cha kwao. Mwa ntchito yake cha kumawa adalawira wa pamseu. Adapeza mkulu wina namfunsa akupita kuti ndipo adayankha akupita kuntchito.Ali mnjira akuyandikira pafupi ndi manda mkulu uja adamuuza wa kabadza kuti akufuna kutsika. Koma wa kabadza chongotembenuka adaona kuti mkulu uja wasanduka mzukwa. "Ndathokoza akulu, pano nde kwathu...." Wa kabadza adangokoleka basikolo paphewa kulikumba liwiro. #mwamunanjenje
Posted on: Tue, 25 Jun 2013 07:28:27 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015