Mpulumusi wafika wampira. Wafikadi mpulumusi yemwe - TopicsExpress



          

Mpulumusi wafika wampira. Wafikadi mpulumusi yemwe timamudikira uja. Zonadi ndiwe mpulumusi wampira, Kodi udalikuti iwe mpulumusi wathu? Nanga ankakusiyiranji? Sankadziwa kuti ndiwedi wofunikira mumpira? Wafikadi wathu mpulumusi iwe Jaman. Kubwera kwako mu team yathu ya Malawi, Tonse tinkalumphalumpha kufuna iwe, Nalo dziko linkakondwera kumva kuti mpulumusiwe wafikadi. Kodi iwe Fisher chinsisi chako nchotani? Malawi ankalira ndikumangoluza ngati mpulumusiwe kulibe,kodi nanga zinkavuta pati? Ndiwedi wathuwathu mpulumusi wampira kudziko lathu la Malawi. Ndiwedi mbambande Anonga Jaman Fisher Kenani Kondowe. Mpulumusi wathu wafikadi wampira. Zikomo!
Posted on: Sun, 16 Nov 2014 12:45:52 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015