Mudzi wina ku china munali bambo wina wake yemwe anthu - TopicsExpress



          

Mudzi wina ku china munali bambo wina wake yemwe anthu onse amamupatsa ulemu kamba ka Chuma anali nacho.. Panali pa 29 june 2014 pomwe bamboyu anadwa mwa serious ndipo anthu anamunyamulira kuchipatala.Mad otolo anauza achibale kuti bamboyu kofunika timupange operation chifukwa vuto ndi mtima wake.Bambo uja samaziwaso kena kali konse chomwe chimachitika.. Bamboyu anakhala 4 days osadziwa kanthu bcoz anamukomola cholinga amupange bwino operation. Panaili pa 03/07/2014 pomwe anazizimuka..atawona mmene analili bambo uja anafusa- Patient : Zikutheka bwanji kut ndipezeke muno Doctor : Munadwala mwakayakayaka moti tikuchitani operation,muzingoyamika mulungu Manager wapachipatalachi atabweletsa Bill ya treatment..bamb o uja atawelenga Paper ya bill anayamba kulira mosagwilika Manager : Vuto ndichan madala?? Inu simumayenela kulira bcoz ndalama takutchajaniyi ndiyochepa kutengela ndimoyo wanu. Patient : Sindikulira kamba ka ndalama mwanditchajayi and palibe vuto ndipeleka Manager : Nanga vuto ndichan?? Patient : Ndikuzimvela chison kut Yehova wandisunga ine kukhala ndi moyo kuzafika mpaka lero.. Usiku onse samagona,masana onse kuteteza moyo wanga koma ine palibe nditsiku limodzi ndinamuyamika.....koma inu adotolo mwangondipanga operation kwamatsiku ochepa mukunditchaja ndalama koma Yehova kunditeteza amanditetezaku palibe malipilo omwe amafuna kwa ine.... Abale anzanga kodi munayamba mwalingalirapo pa zomwe Mulungu/Allaha amakuchitilan? Kunena chilungamo anthufe timangokhala busy ndikudandaula kamba kamavuto omwe tikukumana nawo like Kusowa ntchito,banja,ndalama..timafika mpaka size yonena kut Mulungu Allah wanditaya..Ayi sichoncho tangoganizani inuyo chikhala kut anali kut wakutayan bwezi inu muatafika tsiku lalero kukuwona kuwalaku?? Just imagine iye samagona usiku onse kuteteza moyo wanu koma ndichani chomwe timamulipila?? Malipilo ake sindalama zomwe timazipeza koma kuwupeleka moyo wathu kut ukhale kachisi wake and muzawona madalitso mmene amapelekela mwakathithi. ABALE ANZANGA MWADZUKATU NDI MPHAMVU INU KUFIKILA LERO KAMBA KA IYE,TATIYENI TIKAMULIPILE IYE MWINI MOYO PANTCHITO AMAGWIRA POPANGA COMMENT MAWU OTI ZIKOMO MBUYE #shng_son
Posted on: Tue, 15 Jul 2014 03:14:50 +0000

Trending Topics




© 2015