Mverani Programe Ya Big Bullets Sports Corner Pa Matindi Fm Lero - TopicsExpress



          

Mverani Programe Ya Big Bullets Sports Corner Pa Matindi Fm Lero Ntawi Ikamati 8:30pm Program Imene Imakhala Ikukamba Nkhani Zotukura Team Yathu Ya Big Bullets Maka Maka Zokhuzana Ndi Sapota Mapeto Yomwe Ili njira imozi yotukulira team yathu monga tose tikuziwa League Ikupita Kumapeto Komaso Tili ndi mwayi oti titha kutenga League imeneyi nde mpofunika kuwalimbikisa ma player athu maka maka kunkhani ya ndalama popeza team ikumadalira kwambili ndalama za sapota mapeto Tiyeni Titenge mbali Potumiza ma sms ochuluka kungolemba mawu okuti BB ndikutumiza ku 1515 Mukatelo mwathandiza team yanu Ya Big Bullets... Komaso Pali mwayi oti mutha kuwina katundu osiyana siyana kuchokera ku kampani yathu ya tnm yomwe imathandizaso League yathu ya tnm
Posted on: Wed, 08 Oct 2014 18:27:45 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015