Mwayenera Yehova kulandira ulemu kamba ka zabwino zonse zimene - TopicsExpress



          

Mwayenera Yehova kulandira ulemu kamba ka zabwino zonse zimene mumachita pa miyoyo yathu, tidali ndani ife popanda inu Ambuye? Ena amene tinabadwa nawo limodzi lero kulibe, sikuti ife tapambana kupezeka ndi moyo ayi.Kumbukirani iwo amene ali mchipatala ndi mndende. Ayanganireni amene ali mmaiko akunja kwa Malawi. Tingoti, Mulungu mwayenera inu nokha kutamandidwa.Tifungatireni mu nthawi imeneyi(Psalms 91vs1-16) Mdzina la Yesu Khristu Amen!
Posted on: Wed, 10 Sep 2014 04:59:07 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015