Mwayi kwama artist aluso koma mumasowa EXPOSURE. Kwabwera RED EYE - TopicsExpress



          

Mwayi kwama artist aluso koma mumasowa EXPOSURE. Kwabwera RED EYE ENTERTAINMENT. Just like their page and u will get more infomation from dare. Red Eye entertaiment ikhala ikupangitsa ma shows all over Malawi 4 example; 15 January at Luwinga Private, 17 january kasungu, monthend Panyanja Private in Nkhatabay etc. Ma artist muli ndimwayi okhala nawo in these shows ngat mwa signidwa ndi Red Eye entertainment. For more info u can also call 0999597248 or 0888464166.
Posted on: Sat, 10 Jan 2015 14:05:36 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015