Mwazuka bwanji Maullets!! - Team yathu ya bullets fc, ndiyimene - TopicsExpress



          

Mwazuka bwanji Maullets!! - Team yathu ya bullets fc, ndiyimene yatenga photo za mbiri mu Tnm super league 2014 award!! Izi za ziwika dzuro utsiku pa mwambo womwe akulu akulu a Tnm, pamodzi ndi woyendetsa league yayikulu dziko muno SULOM, anapangitsa ku Complex Hall mzinda wa Blantyre!!! -best goal keeper Vin khune Gona!! -best Midfieder Dalitso Dimaria Sailes!! -Improved player Victor Vibrey Limbani!! -Player of the players Fisher aNonga Kondowe!! -best Coach Sir Eliya Kananji!!! -Bullets yapeza mphoto 5 pa mphoto 8 zomwe zimaperekedwa ndi Tnm!!! -Izi zikudza pameneso bungwe la Caf ku Egypt lavomereza team yokomayi kuti yipange nawo mpikisano wama club omwe achita bwino mayiko mwawo(champions)!! zimene zikususana ndi zomwe akulu akulu woyendetsa mpira wamiyendo dziko muno , amakamba bullets yitapereka chikalata chopepha bungwe la Caf kuti yitenge nawo gawoi!! -Pakadali pano Bullets yili mu mzinda wa Lilongwe kuka tenga nawo gawo mu bonanza yomwe ya kodzedwa ndi a Masa, ndipo yikumana ndi team ya Civo masana ano !! Komaso bullets yikatengerapo mwayi wowonetsa ma sapota ake zikho zomwe yawina season yangothayi carlsburg ndi Super league!! -Tikuthokoza ma sapota nonse amene munaponya vote , anatimwetsa wamkaka nafe tawamweetsa wamkaka!! Mawa wabwino !! #BNSLM2014!!! Sir Jabu!!!
Posted on: Sat, 20 Dec 2014 03:57:34 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015