NKHANI YA RAHMADAN: Ife monga ma ADMN tinapeza mwayi okumana - TopicsExpress



          

NKHANI YA RAHMADAN: Ife monga ma ADMN tinapeza mwayi okumana ndi EXECUTIVE dzulo ndikuyifunsa za nkhaniyi izi ndi zomwe tayankhidwa. RAMADAHN-Anali ndi ulendo kale obwera ku Malawi pa Holiday ya Mwezi umodzi ndiye poona ndi vuto lomwe tili nalo la Zigoli tinaganiza kuti pa nthawi yimeneyo azizatithandizako kuphunzitsa Team yathu,ELIYA KANANJI tinakamba naye ndipo wavomera kugwira ntchito ndi RAMADAN. Munthuyu tizizamulipilira malo ogona,zakudya ndi Transport zomwe zizakwane K1million. QUESTIONS From Admns ADMN-aGS mwati RAMADAN azakhala mwezi umodzi nanga tikazoona mwezi umodzi ukupitilira iye alibe mdziko muno ife tidzatani? GS-Ndipo zimenezo sizidzatheka chifukwa ife sitingakwanitse kumulipira nkuluyu ndipo iye alipa ntchito yabwino ku RSA. ADMN-Kodi Ndalama yokwana 1million yomupatsa nkuluyu idzachokera kuti bwanji ndalama imeneyo osawapatsa ma player?? GS-Zonse zikatheka ndekuti ifeyo tizasonkherana sitizatenga ndalama ya Team. ADMN-Nanga RAMADANyo akazaphunzitsa Team kwa Mwezi nkupezeka kuti Team sikuchinyabe zigoli simukuona kuti Pamenepa tizakhala kuti tabetsa Ndalama?? GS-Iyayi Ndipo aGS anenetsa kuti palibe Coach amene atachotsedwe ntchito chifukwa chakubwera kwa RAMADAN.
Posted on: Tue, 23 Sep 2014 05:38:52 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015