NKHANI YOMWE IKUVUTA KU MALAWI Ndingokuuzani nkhani iyi;Nthawi - TopicsExpress



          

NKHANI YOMWE IKUVUTA KU MALAWI Ndingokuuzani nkhani iyi;Nthawi ina iliyonse kumalawi kutha kuchitika Refrendum yofuna kwapatsa amalawi mwai osankha pakati pa FEDERATION ndi SECCESION.Mabungwe osiyanasiyana ali kalikiliki kuumiliza boma kuti lipangitse Refrendum kuti amalawi asankhe okha.. 5years iyi Peter saimva kukoma ma pressure akuchuluka..Nanga nawo apakati akati akufuna Central ikhale dziko lapadera,apuma bwino?? Nanga ife aku Eastern tikanena kuti Eastern ikhale dziko lapadera? Peter adzamulamulira ndani?? Kkkkkkk kadzikoko ndikakangono koma kuchuluka zochitika mmalo mopanga chitukuko.. I WILL UPDATE YOU MORE ABOUT REFRENDUM,FEDERATION and SECCESION
Posted on: Thu, 02 Oct 2014 15:15:40 +0000

Trending Topics



/Gente-che-Mass-Effect-4-non-è-manco-uscito-è-già-si-topic-768770313140218">Gente che Mass Effect 4 non è manco uscito è già si
Molt Honorable,Sr. ARTHUR MÁS,PRESIDENT ;de la GENERALITAT de
eaning and toiletry products
The GTO has a stablemate. A 2006 Cadillac STS-V. These are
Canon 1490B001 PFI-301PC Ink Tank CNM1490B001AA CHECK YOUR PRICE!
Booba a été attaqué récemment par Rohff dans son morceau
Improvising is your creative ideas played in the context of moving
T-systems ICT Academy is currently embarking on a recruitment
urgently need those toute USACC 600K daily traffic ‖USA OFFNET
** WHY AM I STILL HERE??** Roxy is an outgoing young lady who has

Recently Viewed Topics




© 2015