NKHAZA ZOMWE ZIMACHITIKA UKAPITA KU CHIPATALA CHA BOMA DENTAL - TopicsExpress



          

NKHAZA ZOMWE ZIMACHITIKA UKAPITA KU CHIPATALA CHA BOMA DENTAL DEPT. 1. Anthu amachosedwa dzino without painkiller. 2. Amachosedwa dzino,kamwa itatupa which is dangerous. 3. If the painkiller has expired,ur nt allowed to complain,amakuuza kutiNDIKUSIYATU,NDITHANDIZE ENA. 4. A teeth which can be refilled amalichotsa,AKUTI NTHAWI YOMATA ALIBE. OUT PATIENT DEPT./OPD. 1. Instead of examinin u,amangolemba mankhwala amene akuwadziwa,NEXT. 2. Munthu sunamalize kunene vuto,amapezeka alemba kale.. Anthu ambiri amapatsidwa mankhawala olakwika. 3. Instead of first come,first save they wil attend their friends,or they wil assist u while she is on a Cell phone. EMERGENCY ROOM/KUNGOZI. Instead of helping u with love and kindness,umafunsidwa mafuso while ur losing blood and ur in Pain.... IN PATIENT/WARD. Anthu ovutika,opanda dzina or abale,they are treated like in hell. 1. A patient is ordered to clean masanzi or magazi. 2. Cleaner can b the one giving u med attention while ma nurse akucheza. 3. Drip amakuika ndi cleaner while ma nurse akucheza. 4. They wil attend at u as if ur enemies,osakusekerera,and u ask ursef. NDA ALAKWILA CHANI A SISTER. MATERNITY WARD/LABOUR. Another hell in govt hosp. U wil come alive or dead. 1. They wil shout at u while in pain,UKWAWAUZE AMUNA AKOWO ABWELE ADZAKUCHIZE. 2. Ana ena akubadwa opundukawa its nurses,to blame instead of supporting u,amangokuyangana. 3. Ana akumwalira ku labour its nurses to blame. 4. Most women are dying in labour,ma nurse zosawakhuza. ZINA ZITI ZOMWE TAIWALA APA?
Posted on: Wed, 09 Jul 2014 06:16:53 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015