NTCHITO ZA M`KABUDULA MWANGA KUCHITILA UMBONI. Akuluakulu - TopicsExpress



          

NTCHITO ZA M`KABUDULA MWANGA KUCHITILA UMBONI. Akuluakulu wandibwelesela mwana dzulo madzulo #Nomsa yu! Ku room yomwe ndimakhala ati ndi wanga eti?komatu thawi zambili timagwilisa ntchito ma condom pogonana! Tsono ndikuopa kuti ndimukanile!“eyi azangondimangisa” Ndiye akuti ndimutche dzina!Ena awiri mukuwaonawo ndi angaso aku Malawi amkadzi wanga Nanjele,{komatu zovala thawi zina ndimawatumizila koma mudziwa anawa kusasamala} maina awo ndi Ganizani winayo Fanizani,Ndithandizeni abale anga mwa Ambuye ameneyu ndiye ndimutche dzina loti ndani?
Posted on: Tue, 15 Jul 2014 23:26:59 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015