Ndikumalawi kokha kumene munthu umakhala oyipa ukakana kulowa - TopicsExpress



          

Ndikumalawi kokha kumene munthu umakhala oyipa ukakana kulowa riddim yamunthu winawake eish.. Ineyo sinditha kuyimba mmene mumanenera koma I knw how far I want to go with music. And I knw standard ya musik imene ndimafuna... Ndiye ndikapanda kulowa instrumental yanu chisakhale chifukwa chomandinyozera... Kodi mumafuna every riddim yatuluka ndilowe? Nde ndiziimba mbweleratu.... Anthu ambiri amene amalowa every riddim ikatuluka saimba zolongosoka... Take yoh time... Ine ndine osatha kuimba thats why ndimatenga nthawi pofuna kuimba zolongosokako.. Mwina nkuzafika pa amene mumawafunawo. Rahtatatatata ah guh blaze Malawi 1day... And muzakhala mukumandinyengelera kuti ndizalowe ma studio anuwo.... Nde muzisamala poyankhula my coz my present situation is not my final destination
Posted on: Tue, 07 Oct 2014 10:24:57 +0000

Trending Topics



Its good to leave the stage when the ovasion is high has it a wise
Skuad Chelsea Tur Asia 2013 Post by Alfarenza 1. Petr Cech 2.
Mud slinging continues. Many assume that Curacaos elite is deeply
Rozpis zápasov II.B trieda 2013 / 2014 1. kolo 4.8.13

Recently Viewed Topics




© 2015