Ndine oyimba osatchuka. Mwina mutha kumafunsa (why) ndili oyimba - TopicsExpress



          

Ndine oyimba osatchuka. Mwina mutha kumafunsa (why) ndili oyimba osatchuka? Mchaka cha 2008 ndinatulusa chimbale chomwe chinagudwa ku USA ndi ku RSA Mwayi otchuka udalipo koma ine sindimkafuna kukhala oyimbachabe ndimkafuna kukhala ndi studio yangayanga osati ndizipita kumastudios ainuake ai. Panopa ndikhala ndi studio yanga Komanso zida za u DJ. Ku MALAWI. Ikhala studio yosalipila(ulele) ukakhala ndi funso funsa ndipo ika 4n Number ndi 4na. Victor Nazombe, Mr Gray Samani akundiziwa.
Posted on: Tue, 27 Aug 2013 18:31:58 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015