Nkhani yangotipeza kumene, team ya Wanderers ikufuna kutumiza ma - TopicsExpress



          

Nkhani yangotipeza kumene, team ya Wanderers ikufuna kutumiza ma players 5 ku Wanderers Youth, maina awo ndi awa: Omega Mhone, Develious Mwale, William Abudullah, Felix Katongo and Diverson Chilemba. Akuti malipiro awo sasintha akapita ku Youth ko. Inu maganizo anu ndiwotani?? Is that a good decision? Ndipo team yi ikufuna kumpatsa contract Elijah amene wachokela ku Nkhata-Bay , ndi stricker. Once anomad alwez awanderer wise pples choice. TROX, Mtsikana woyikonda Noma, jersey No 2
Posted on: Sun, 10 Aug 2014 16:58:57 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015