Nw zimandivetsa chisoni chakuti anthu mumasiya dziko - TopicsExpress



          

Nw zimandivetsa chisoni chakuti anthu mumasiya dziko lako kupita dziko lawini ndicholinga choti uchepetse mamvuto. Panali nyamata wina adapita ku jubeck mwachisomo adayamba ganyu. Kma zovetsa chisoni chakuti adapeza ndalama yokwana R2000 iye wayitenga ndalamayo wathawa nayo. Mafuso akubwera kuti ndalama imeneyi imuthandiza chiyani si minyama imeneyi. Mmene report likubwera likunena kuti tsono ali ku Malawi ndi R2000.
Posted on: Mon, 26 Aug 2013 18:14:29 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015