Okay I know we have to move on and its kinda uncool to diss the - TopicsExpress



          

Okay I know we have to move on and its kinda uncool to diss the the other competitors who lost the Presidential bid. So believe me this will be my only jab at you okay? Nanga ndingokusiyani choncho? Zosatheka! Hihihi!! Eeeh. Nde inuyo zoona maka a PP mukakhala mumaganiza zoona kuti amayi amene aja angawine?! Zoona?!! Olo kutikoo? Nanunso you were too ambitious. Kenakano ndeno inuyo inu a MCP zoona munthu amayendetsa chalichi nde mumati angayendetse boma?!! Boma mumalidziwa inuu?!!! Mmmm. Ndeno munthuyo akhale wa American accent aissh! Zero mama. Finally no inuyo a UDF. Kupepetulidwa chani?! Zoona kungomva kuti mwana wa former Pulezidenti basi inu yemweeyo! Kufunsa kuti ma achievements ake ndi chani? Zero. Za daddy basi!!! Kikikiki! Osakwiyatu mwamva?!!! I love you all. Koma muzikhala osova!!! Ma calculator mmanja all the time. Okay! ?!! Hihihhihi! Basi sindilembanso za mwano. #ndakunjoyanibeni!!!
Posted on: Sat, 31 May 2014 12:08:59 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015