PEMPHERO LA LERO Titseke maso tipephere. Oyera oyera mulumgu - TopicsExpress



          

PEMPHERO LA LERO Titseke maso tipephere. Oyera oyera mulumgu wakumwamba,zikomo kwambiri potidzutsanso ife lero ndi moyo siife opambana koma mwatikondera tsiku lalero kuti tikanthe kuona kuluzanso kwa bullets lero,chonde mulungu wanga idalitseni Blue Eagles pamene ikusewera lero kuti ikathe kupambana pa masewero ake masanawa,kapatseni mphamvu anyamatawa asakafooke mpaka kumapeto,paja odzikweza mumamutsitsa,ndipo odzitsitsa mumamukweza,choncho BLUE EAGLES Yadza pamaso panu modzichepetsa ndi modekha. . .ndikudziwa kuti tahiti bullets singawine. Muzi la tate ndipemphera..AMEN!!!
Posted on: Sun, 25 Aug 2013 05:25:46 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015