Pakadali pano tili ndi ma Admi awiri Mayi awo ndi awa #Wak_boy ndi - TopicsExpress



          

Pakadali pano tili ndi ma Admi awiri Mayi awo ndi awa #Wak_boy ndi #k_sis........Tikufuna ena 6 kuti tisangalatse anthu akuno ku mponela ndiye pali funso amene ayankhe bwino timusankha kukhala Admin funso lili chonchi-----------------------------Pamene iye anali ndizaka 5,Mkulu wake anali ali ndi Zaka 10..Panopa iyeyo ali ndiZaka 20 ndiye kuti wangonoyu panopa ali ndi Zaka zingati?..........Legooooooo!!!! #K_sis
Posted on: Wed, 27 Nov 2013 17:03:16 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015