Pamene masiku apitawo zinadziwika kuti ROBERT NGAMBI sakhala nawo - TopicsExpress



          

Pamene masiku apitawo zinadziwika kuti ROBERT NGAMBI sakhala nawo pamasewero a Malawi ndi Benin Loweruka lino, zadziwikanso kuti ESSAU KANYENDA komanso ATUSAYE NYONDO sakhalanso nawo kamba kakutangwanika ndimatimu awo mdziko la South Africa. Pakadali pano osewera amene afika kale mdziko muno ndi JOSEPH KAMWENDO, CHIMANGO KAIRA, CHIUKEPO MSOWOYA komanso ROBIN NGALANDE. GABADINHO MHANGO komanso LIMBIKANI MZAVA akuyembekezeka kufika loweruka lomwelo kuchoka ku South Africa. #VIVAFLAMES
Posted on: Thu, 31 Jul 2014 07:04:04 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015