Sports - TopicsExpress



          

Sports Update!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Mpira Ulipati????????????? Ena akumafusa kuti kodi nkhani ya mzungu akudzakocha Malawi uja sakuimvetsa bwino:Nkhani yake ndi yoti mzunguyu Tom saintfeit yemwe kwao ndi ku Belgium anachita kupempha ku Fam kuti poti iyeyo Nigeria anagwilapo nayo ntchito akuidziwa kufooka kwake nde ampatse mwai oti aithandize Malawi,koma akadzawina azamuganizile kumulemba ntchito ngati permanent coach,Nde a Fam anamuuza kuti ife ndalama tilibe,nde iyeyo anangoti aa chabwino olo salary musamandipase muzingondipasa transport,zakudya ndi malo ogona.Mpamene a Fam ankavomela,ndi mmene zinakhaliratu,moti mawa awonela nawo ya Mozambique pa civo,sabata ya mawa ku ali ndi anyamata wa ku cosafa kenako azizakonzekela bwino za Nigeria,usiku wa bwino kwa nonse.
Posted on: Fri, 05 Jul 2013 20:26:44 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015