TICHEZE TSOPANO Dziko lathu la malawi talamulidwa ndatsogoleri - TopicsExpress



          

TICHEZE TSOPANO Dziko lathu la malawi talamulidwa ndatsogoleri okwana 4,alipoyu wa nambala 5...Komano mwatsogoleri onsewa alipo amene inu amakusangalatsani muulamuliro wake moti simudzamuiwala mpaka kalekale... NDINDANI AMENE MUMAMUFILA MPAKA PANO PA MAINA AWA; 1=Dr Hastings Kamuzu Banda(1964-1994,,17may) 2=Dr Bakili Elson Muluzi(18may 1994-2004,19may) 3=Dr Bingu Wa Mutharika(20may 2004-2012,,5April) 4=Dr Joice Hilda Abiti Mthila Banda(6April 2012-2014,,,20may) 5=Prof Peter Athur Mthanyula Mutharika(Active Now) WANU ALI PATI????? kkkkkkkkkkkk WANGA NDI NUMBER 4....
Posted on: Mon, 03 Nov 2014 06:31:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015