TIKUFUNA KUSEWERA FRIENDLY NDI MAMELOD SUNDOWNS -#FOTE: Pamene - TopicsExpress



          

TIKUFUNA KUSEWERA FRIENDLY NDI MAMELOD SUNDOWNS -#FOTE: Pamene tikukhonzekera nkhondo ya mu caf yomwe ife mapale tayishosha, excutive yathu motsogozedwa ndi a chair Kondie Msungama, atikonzera ma sewero opimana mphamvu ndi timu ya ku south africa ya mamelodi sundowns omwenso ndi ma defending champions a absa premier ligi ya mu season ya 2013-2014. Malingana ndi harold fote yemwe ndi mlembi wa bullets fc, wati bullets iseweranso masewero enanso ongopina mphamvu ndi ma team ochokera ku maiko monga tanzania, mozambique komanso zambia ndipo kuti izi zichitika tisanasewere masewero athu oyamba a mu caf ndi timu ya fomboni. Fote wati mamelod sundowns yavomereza kubwera kuno ku malawi cha mkati kati mwa mwezi omweu wa january. Paza osewera omwe bullets ikale igula fote anati zonse zili nchimake ndipo kuti pomafika pa 31 mwezi uno mapale akhale akudziwa kti ndi ma player ati omwe akubwera ku bullets. Ma pale nkhani ndi imeneyo excutive yathu ikutibweretsera Mamelod sundowns inu mukuilandira bwanji nkhani yabwinoyi? #BNSLM2014!! FRAZER
Posted on: Thu, 25 Dec 2014 05:38:44 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015