TIKULILA S.A.B.C NDIMA CHANEL ENA OMWE ASOWA LELO! zikomo mkonzi, - TopicsExpress



          

TIKULILA S.A.B.C NDIMA CHANEL ENA OMWE ASOWA LELO! zikomo mkonzi, Ine ndi arberto nkulinga yemwe pakadali pano ndikukhala ku south Africa. Ndangomva kuti boma lakuno lachotseratu wayilesi yao ya Boma ya S.A.B.C. Ku malawiko. Izi zandinyasa kwambiri monga mzika yakumeneko. Kodi akuona ngati ndife otsalira eti? Aona tibweretsa ma Chanel athu apa free to air adziwenso kuti ndife osafanana nawo. Amalengezatu kunoko! Amvekere- kuwina kwa Brazil kwathawitsa S.A.B.C kutimayiko tingapo! Apange yao nawo. Zikundipweteka kwambiri!
Posted on: Mon, 01 Jul 2013 18:51:35 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015