TIKULINGALIRA ZOSEWELA MU CAF-FOTE Mulembi wa mkulu wa team ya - TopicsExpress



          

TIKULINGALIRA ZOSEWELA MU CAF-FOTE Mulembi wa mkulu wa team ya Bullets Harold Fote wati team yi ikulingalira zosewela nawo mu mpikisano uja wa Caf ngati Bullets ingatenge chikho cha TNM super league, Fote wati Team yi iriso ndimalingalilo owonjezela osewela ake pomwe afote anatchula player wa Sliver strikers #Chawanangwa_Kawonga yemwe iwo ati akumufuna ndipo awona mmene angachitire League ikatha. #zex1
Posted on: Fri, 24 Oct 2014 05:23:42 +0000

Trending Topics



be-topic-10152743841349928">Spectacular filly Untapable and jockey Rosie Napravnik will be
Why is it that the Nigeria anti sodomy (gay) law sign by president
New Entry #39 DEEJAYWORX-WORLD-CHARTS DJ Rob de Blank - SHE

Recently Viewed Topics




© 2015