TIWERENGANSO MA VOTE A KU LILONGWE CITY SOUTH EAST CONSTITUENCY - - TopicsExpress



          

TIWERENGANSO MA VOTE A KU LILONGWE CITY SOUTH EAST CONSTITUENCY - MALAWI ELECTORAL COMMISSION Bungwe la MEC likudziwitsa a Malawi kuti la chiwiri lino (pa 8 July 2014) likhala likuwerenganso ma vote a ama MP ku constituency ya ku Lilongwe City South East chifukwa a court awalamula kutero A MEC adapanga declare kuti Honorable Namasasu a chipani cha DPP adawina koma candidate yemwe amayimila MCP, bambo Ulemu Msungama, adakapanga challenge ma results wo ku court chifukwa malinga ndi iwo akuti ma results ali nawo amawonetsa kuti adawina Ndiye kuwerenganso ma vote ku kukhalako Tuesday likubwelerali
Posted on: Sun, 06 Jul 2014 04:30:00 +0000

© 2015