Team ya Blantyre united yatuluka mu superleague lero yitapanga - TopicsExpress



          

Team ya Blantyre united yatuluka mu superleague lero yitapanga draw ndi team ya Mafco!! Blantyre united ndi team yomwe bullets yikuyenera kuyithokoza kwambiri potengera kuti malonda awo ndi Bullets pama players amayenda mosavuta!!! Victor Limbani!! Dalitso Sailes!! Tizgowere kumwenda!! Awa ndi ena mwa maplayers amene anabwera ku bullets pa ngongole ndipo later anagulisidwa ku bullets , mateam awiriwa atakhala pansi!! Ife monga Maullets , amene thawi zonse timathokoza zomwe ma team ena amatipangira monga team yayikulu MMalawi muno!! Tikugofunira zabwino Blantyre united ndipo Tili nacho chikhulupiliro kuti Mr Nakoma ndi gulu lawo ayetsesa kuti teamuyi yisathe!!! Mwakoma Nonse!! #BNSLM!!!! Sir Jabu!!!
Posted on: Sun, 23 Nov 2014 16:16:02 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015