The New ministers,campaign director,govenor and IG inspector - TopicsExpress



          

The New ministers,campaign director,govenor and IG inspector general alumbilitsidwa masana ano ndipomwe Mr presdent atiwuze maganizo awo,PPP inayamba chaka cha 2006 pa 22 may...oyambira kulowa guluri anali George Ngwazi Mapopa Tembo,Norman Chikaphupha,San B ndimene amka joimer sydney mpofu ndi ena ambiri koma mwa ena omwe analipo palibepo pano chifukwa chodzikweza ndi kudzitamandira pa okha anachotsedwa..pakali pano ili ndi ma member 300 something-omwe ena akufuna apungulidwe masana ano.Ine Elizah ndi nalilowa gululi 2011 nditasi ntchito ya nurse ku Queens hopital ndibwera kuno south africa ndipomwe ndina dziwa facebook,iyi ndi mbiri ya PPP..mutha kuona nokha kut zaka zomwe yatha PPP ndi 9yrs yakhala ikutukula anthu munjira zosiyanasiyana kut ndinene mudzati ndi kukumba mpando wa PPP ulibe mwinimwini udindo muli nawowo enaso anali pompo kumangofunika ndi kucheza mwa bata palibe yemwe amalandira ndalama zocheza izi ngat chibwenzi kapena masanje kut mukudikira mudzalowe banja kukhala bambo or mayi odalilika,kucheza uku ndikuthandizana PPP real ever
Posted on: Sat, 06 Dec 2014 08:40:47 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015