Timu ya big bullets ikhoza kuchotsedwa mu mpikisano wa caf ngati - TopicsExpress



          

Timu ya big bullets ikhoza kuchotsedwa mu mpikisano wa caf ngati timu ya silver siingalole kugulitsa chawanangwa kaonga poti a bullets atumiza kale ku caf dzina la chawanangwa,malamulo a caf amati kulembetsa dzina la player emwe siwanu chilango chake timuyo amaichotsa ndi kuilipilitsa ndalama zokwana 150 million,koma a silver akunenetsa mawu awa(chawanangwa is not 4sale) kaya tiziona mmene zithele,happy new year!.
Posted on: Thu, 01 Jan 2015 14:04:20 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015