Tsiku lina Bengo anapita ku supermarket anapeza zokudya za a - TopicsExpress



          

Tsiku lina Bengo anapita ku supermarket anapeza zokudya za a mphaka akugulisa pa low price ndipo anatenga dozen .manager poona anaganiza kuti Bengo alibe mphaka ndipo afuna akadye ndi ana ake ,ndipo adamuuza kuti akatenge mphaka ngati umboni .bengo mosanyozera anakatenga ndipo anamulora kugula dozen ija.. Tsiku linanso anakapeza zokudya za agalu zitatsikanso mtengo ndipo anatenganso dozen .manager ujanso anamuuzanso kuti akatenge galu yo ngati umboni ndipo anakabwera naye wagulanso.. Tsiku lina anafika ku supermarket kuja atatenga chikwama cha mmanja ndipo anangofika straight kwa manager uja Bengo: hello bwana tapitsani nchikwamamu Ndipo bwana uja mosanyozera anapitsa Ndipo ananva ngati phala phala Manager: (monyasitsa nkhope)kodi ndi manyi eti? Bengo:akumwetulira)eeee ya Manager: (mokalipa)tsono bwanji ukundigwiritsa ine ndalakwa chani ? Bengo : ndufuna kugula ma toilet papper ndiye ndangokubweretseranitu manyiwa kuti ndisabwererenso kukatenga umboni
Posted on: Tue, 08 Jul 2014 14:05:18 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015