UPDATE: Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) has maintained - TopicsExpress



          

UPDATE: Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) has maintained pump prices for fuel. Petrol will still be sold at K839/litre and Diesel at K853.40/litre. --------------------- Bungwe la Mera lati silikweza kapena kutsitsa mtengo wa mafuta agalimoto komanso a paraffin mwezi uno. Zikatere mitengo yonse yamafuta siyisintha moti petulo akugulitsidwabe pa mtengo omwe uja wa K839 pa lita, dizilo pa K853 ndipo mafuta oyatsila kaliboli (nyali) akugulidwabe pa K719.30 pa lita.
Posted on: Thu, 14 Aug 2014 05:51:23 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015