Watch out this Kunali chimsonkhano cha azipongozi(by this I - TopicsExpress



          

Watch out this Kunali chimsonkhano cha azipongozi(by this I mean mayi ake amamuna ndi mkazi wake wa mwana wawo/ mother in law and daughter in law) Anthu onsewa anatengedwa pa ma bus makolo bus yawo yawo,,azikazi a ana awo nawonso bus yawo ulendo opita ku malo amsonkhano! Bus ya atsikana ndiimene idayambilira kufika ku malo kuja...and patapita nthawi akuluakulu ochititsa msonkhano adalengeza kuti kwachitika nkhani yoopsa bus ya azipongozi(makolo)yachita ngozi ndipo makolo onse afela pomwepo.. Atsikana aja adayamba kusangalala,kuvina kunyadira za imfayi except mtsikana mmodzi yekha yemwe amalira kwambiri mosatonthozeka! Anzake anamufunsa kuti nanga iwe ukulira chani? AmvekereApongozi anga anachedwa ndiye bus yaathawa 3 minutes ago Like · Comment · Share Hide
Posted on: Fri, 08 Nov 2013 16:52:59 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015