Wisest pipo mtsikana wankhani ya dzulo wathandizika. The gal has - TopicsExpress



          

Wisest pipo mtsikana wankhani ya dzulo wathandizika. The gal has made up her mind to disclose her HIV status to her boyfriend yekha. She isnt doing it today, akuti amuuza next week so that akonzeke psychologically, Ngati boyfriend sazamvetsa, azamupempha kuti apita onse for HTC. Thanks guyz. You are a blessing. Leronso kuli ina; I am 20 years old, married and Ihave a child. Ndinalowa mbanja mwachangu because ndinatenga mimba nde boyfriend wanga anangoti tikwatirane after all kwathu mai anga ankandinyoza nde I decided kuti ndimvere boyfriend wanga. Bestfriend wanga wakhala akumandithandiza ndi ndalama komanso zovala because mwamuna wanga panopa sakumandigulira zofunikira even maunits ndimachita kuvutikira kuti ndipeze. Some months ago, I realised kuti zovala ndi ndalama wakhala akundipatsa bestfriend wanga nzochokera kwa mnyamata wina wake amane wakhala akundifuna kuyambira ndili form 1. Mnzangayo anandikakamiza kuti ndigone naye mnyamatayo pomuthokoza pa zonse wakhala akundichitira. Ndinagona naye. Panopa mnzangayo akumabweretsanso zinthu zina ndipo zikumakhala zofunikira pakhomo because mamuna wanga doesnt care about me and my child. Mnzangayo wandiuza kuti ndizingolandira kuti timudyere mnyamatayo koma ndikuopa at the same time ndikufunika thandizo for my child. Mamuna wanga ali ndi barbar shop koma akandipatsa ndalama patsiku ndi K1000 basi, daily kumangoti business yavuta. Zimenezi zikundiika pa mpanipani, nditani?
Posted on: Tue, 14 Oct 2014 07:50:20 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015