ZAMANYAZI KWAMBIRI Player wa Silver Strikers, Peter Pindani, - TopicsExpress



          

ZAMANYAZI KWAMBIRI Player wa Silver Strikers, Peter Pindani, omwe omunyadila amati Pidoh wamangidwa ndi a police kamba kokuba katundu mu shoprite ya ku Lilongwe osalipila. Izizi ndi zamanyazi kwambiri kutengera kuti a Pidoh ndi graduate wa ku Chancellor College. Kapena amawona ngati hassle? Ma report akuti a Pidoh anamenya Deal ndi cashier wa shoprite kuti abe katundu yo. Ndipo wa G4S ndi amene adawagwira anthuwa
Posted on: Tue, 20 Jan 2015 16:54:46 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015