ZINTHU ZOMWE ZINATHA FASHO 1. Kufusiridwa nkumuyankha - TopicsExpress



          

ZINTHU ZOMWE ZINATHA FASHO 1. Kufusiridwa nkumuyankha kuti ndikuyankha mmawa,,,pano ndi pompo pompo... 2. Kumenyanirana mwamuna kapena mkazi.. 3. Banja or chibwenzi chikatha mkumamuyalutsa mnzako pa fb... 4. Kufuna kutchuka chifukwa cha ndeu 5. Kufunsilira mkazi mphamvu.. 6. Kumenya mkazi.. 7. Kuuza anthu pa facebook chibwenzi chatha.. 8. Kupita kwa TB Joshua.. 9. Zokuba ma bed.. 10. Zomalemba status yoti,ine ku inbox ayi... 11. Zopanga edit foto kuziika limodzi ndi kambutuma kako.. 12. Zomamva kuti flames yaluza... Wonjezerani zina... #advisor02
Posted on: Sat, 02 Aug 2014 17:41:37 +0000

Trending Topics



: drums,

Recently Viewed Topics




© 2015