Zomwe zingakupangitseni kuti mudziwe kuti nkazi ali ndi zibwenzi - TopicsExpress



          

Zomwe zingakupangitseni kuti mudziwe kuti nkazi ali ndi zibwenzi zambili pa facebook pano........ 1. Amakonda kumalemba ma status monga missing u honey koma osalemba dzina la munthu amene amusowayo 2. Amakondanso kumalemba zoti i love him kaya amati ife tiziti amakonda ndani... 3. Ukakhala nawo pa chibwenzi safuna kukupatsa password yawo amanamizira zoti ananditsegulirandi brother wanga nde password sindikuiziwa...... 4. Safuna kuti uzipanga comment photo kapena status yawo, ukazipangira mwa iwe wekha sakuyankha... 5. Ukapanga comment pa photo kapena status yawo amadikila wina apangenso comment then amayankha kuti thanks guys 6. Ukapanga comment kuti nice looks honey amayankha kuti thanks dear kapena kui deleter comment yakoyo... 7. Amanamizira kuti ndili ndi azibale ambiri pa facebook pano nde usalembe zoti in relationship with me undiika mmavuto.... 8. Mnyamata wina aliyense amakhala brother kapena cousin nthawi zina school mate wawo.... 9. Iwe ukawalembera message yoti i love u imatenga nthawi kuti ayiyankhe kenako kuyankha kwake amangoti ok. 10 ngati muli ndi zina onjezerani #Brizzy
Posted on: Sun, 04 Jan 2015 11:06:45 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015