Zoti kuli Edzi mukudziwa ndinu anzanu ena simmene akuuyikira moyo - TopicsExpress



          

Zoti kuli Edzi mukudziwa ndinu anzanu ena simmene akuuyikira moyo wawo pachiswe, zachisoni mukatenga matendawo mumalemba ena ntchito yoti azikudwazikani. MOKUPEMPHANI Enanu ndiapabanja koma kuyenda kuipa nthawi zonse ndipo muli ndi zibwenzi zambirimbiri pali inupo, bwanji mukazayamba kudwala komakandakanda, kudwala komanyeredwanyeredwa, kudwala komansanzansanza, kudwala komakhosomolakhosomola, muzakhale kudambwe komweko komwe mwapala motowo osati wachikondi wako uzamusowese mtendere panyumba ndichibwana chako, ndiwe opusa chibwana chako chizakulange basi munthuwe. POMALIZA Musandine ine ndi otumidwa koma ngati munganene kuti ndi chipongwe kapena mwano si ine amene ndili ndimwano koma amene anditumawo ndiye ali ndi mwano. Koma ngati mukuti ndili ndi nsambi mulakwitsaso monga ndanena kale ine ndangotumidwa wansambi ndi amene amati ndimuyakhulire kumitundu ya anthu.
Posted on: Thu, 04 Dec 2014 21:41:12 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015