ife man ndi aku Dedza kasumbu Roard man! musavutike ndikufunsa. - TopicsExpress



          

ife man ndi aku Dedza kasumbu Roard man! musavutike ndikufunsa. Dedza ndiboma man lonyumwitsa dedza post between mozambique you can see here my profile picture alise waku Dedza ndidolo man! why? mufunse akuzani man udolo wake inu simungauziwe.man inuyo kungofika dedza kasumbu Roard ndikufusa kuti kodi nyamata uja you khobodoza man fintenation pack Airport toilents tiyanjane shorp forward here chapompapa man!hahahahahahahahahahahahaha umaziwa yam,bunoija man zina ukamanva ngati ukulota,zina ukawona kambanga mwala,wapachara ndiwaphepo,wako ndiamene alipamphuno,amatelo kaya! wako ndi amene ulinaye pompo,alikutali ndi wayena,ukatambatamba uziyangana kumwamba/kum,mawa because kungakuchere ungayende osanvara kukafika kwapongozi ako.njara ikakupora umafuna kudya,ukadya umafuna madzi yoti umwere pazakudya zimene wadya,after that umazapita kumalo otamandika kwambiri kuti uwone kusitha zaday yarelo,usaiwale kuti unabadwa ndipo pano ukuyembekezera kufa wina aliyese akuyembekeza tsiku lopambanari kuti machimo athu amene takhara tikudzibisa pano padziko lapansi akaululuke,pano tikubisa koma kumwamba akakhara pamwamba patsindwi ranyu akujowajowa,akuwambidwa ndi sun malingana ndintchito zake zimene mukugwira dziko raeni ake kuti azanu asapeze ntendere.hahaha ok tikumaneso 12:pm muno.
Posted on: Fri, 19 Sep 2014 09:24:37 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015