Hahahahaha!!!! Abwana anatenga wantchito wawo ku Mount Soche for - TopicsExpress



          

Hahahahaha!!!! Abwana anatenga wantchito wawo ku Mount Soche for lunch ndiye anamuuza kuti chimene adzichita bwanayo wantchitoyo adzichita zomwezo,ndiye anadya ndikumaliza. Atatha bwana anatola tooth pick nayenso wantchito anatola yake, ndiye atafika kunyumba bwana anafunsa wantchito uja kuti wainjoya bwanji lunch iye anati," lunch ija inali bwino koma mwandipweteka pomeza kamtengo komaliza kaja".
Posted on: Thu, 26 Sep 2013 06:30:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015