KU LILONGWE NDI DEAL Ndalama zokwana 11 million kwacha ndi - TopicsExpress



          

KU LILONGWE NDI DEAL Ndalama zokwana 11 million kwacha ndi zomwe zinapezeka pa masewera a pakati pa Wanderers ndi Bullets ndipo ma team anapatsidwa 2.5 million Kwacha. Mlembi wamkulu wa Sulom Williams Banda wati izi zimasiyana ndi ndalama zimene zimapezeka ku Blantyre ngakhale kuti ku Blantyre amasonkhana anthu ambiri ndipo wati akuyenera kusintha njira zotolera ndalama ku Blantyre. Ku Lilongwe, bungwe la FAMA ndi lomwe limatolera ndalama pamene ku Blantyre, masapota amakhala okha mma gate kutolera ndalama. Ku Lilongwe kuli bwino kwambiri........@Andy (the undisputed)
Posted on: Mon, 02 Dec 2013 05:22:34 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015