KUKWIYA>> mnyamata wina wa mmudzi wa Sanjani ku Mneno - TopicsExpress



          

KUKWIYA>> mnyamata wina wa mmudzi wa Sanjani ku Mneno anagwirilira mlongo wake amene ali wa zaka zisanu pamene mnyamatayu ndiwazaka 21, wakhala mu chitokosi kwa masiku atatu kenako anakaonekera ku khoti ndipo anamulamula akakhale ku ndende miyezi 9 pomwe izi zimachitika bambo anali ali ku Mozambique lero atangofika anapita kukamuona mwana wao ku ndende koma achitetezo apandendepo anali odabwa pamene bambo amamenya mwana wawoyo molimbika iwo anati chigamulocho chachepa chifukwa atopa naye mwanayo
Posted on: Fri, 03 Oct 2014 15:17:17 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015