Kumudzi kuno zinthu zikusintha tsiku lililonse, mwa zina - TopicsExpress



          

Kumudzi kuno zinthu zikusintha tsiku lililonse, mwa zina chiyankhulo chikusintha pangono pangono; onani Chichewa ichi momwe chasinthira: 1. Phokonyole -> Mkazi wosaoneka bwino 2. Mponela -> Mkazi wa mbina yabwino/wokongola 3. MASM -> Nsima ya mmamawa yokhuthula/yopanda mitanda 4. Wakwera Tata -> Akumwa ma ARV 5. Bush Doctor -> Wogulitsa Chamba/fodya wa mkulu 6. Dzombe -> munthu woledzera mowa ogula ena 7. Defensive Mechanism -> mbuyo ya mkazi 8. Attacking Force -> Mabere/chidali cha mkazi 9. 2 SIM Card -> Mkazi wonenepetsa 10. Kanengo - Zachimidzi/ zovala za achikumbe akaguitsa fodya ku Kanengo 11. Joe Gwaladi -> Ma silipasi/sandals/Lafutasi za plastic 12. Wrong Turn -> mkazi osawoneka bwino 13. Tahiti -> Mkazi wokonda kunyengetsa 14. Merchant -> munthu amene amagulira anzake mowa 15. Blackberry -> Munthu wokuda kwambiri 16. Chokonoka -> Mkazi osachedwa mimba 17. Gaddafi -> Maliseche a mwamuna 18. Ndata -> Maliseche a Mkazi 19. Bwenje -> mkazi wa ndata yayikulu 20. DJ -> wantchito wa panyumba 21. JB -> Mkazi wa panyumba 22. JB -> Jumbo ya Bonya (Usipa) 23. PP -> Zinthu zosaoneka tsogolo lake 24. China -> Zosalimba/zabodza/zopanda pake/ za fake 25. Yabooka -> mkazi wonyengetsa kwa aliyens
Posted on: Sat, 09 Nov 2013 16:27:17 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015