MUNGAMUTHANDIZE BWANJI MUNTHUYU GUYS?? Admin musabise dzina langa - TopicsExpress



          

MUNGAMUTHANDIZE BWANJI MUNTHUYU GUYS?? Admin musabise dzina langa yi. Ineyo ndimakhala kunoko ku Area 18A. Kwa neba anga kuli grocery imene mumakhala zinthu zosiyanasiyana ngati ma units, chishango, mankhwala a panado, ma fanta ndi zina. Vuto langa nali. Chimandidabwitsa mchoti ndikapita kukagula zinthu, kenako kupeleka ndalama amakonda kunena kuti change alibe. Kupeleka K1000 change palibe Ukapeleka K500, umva change palibe Kupelekanso pena K200 umva change palibe Tsono amafuna kuti ifeyo tizisiya change cho coz zoti titenge pa ngongole amakana. Inetu izi sizimandiwazayi. Kuli bwino ka grocery kawoka angotseka ife tiwona kolowera. Vincent Chirwa Kanyisko Area 18 LL
Posted on: Mon, 07 Oct 2013 17:47:11 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015