Mwana wamoya adabwera akulira mosatonthozeka Moya:chavuta ndi - TopicsExpress



          

Mwana wamoya adabwera akulira mosatonthozeka Moya:chavuta ndi chani mwana wanga? MWANA:adad kodi ineyo ndimaoneka ngati mfiti kapena chosanduka? MOYA:Ayi MWANA:Maso anga ngotudzuka ngati a birimankhwe? MOYA:Ayi MWANA:Mutu wanga ngopowanizika ngati naligonkhwiro? MOYA:Ayi MWANA:Ndimakhala ngati ndine wamisara kapena ndinagwerako mtoilet? MOYA:Ayi,udabadwa bwinobwino mwana wanga MWANA:Nanga bwanji anthu amati ndinafanana nanu?
Posted on: Sat, 24 Jan 2015 18:49:35 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015