Ndi mtima osweka ndati ndikutsineni khutu kti lelo conductor wa - TopicsExpress



          

Ndi mtima osweka ndati ndikutsineni khutu kti lelo conductor wa bus wa mwalira chitseko chitatseguka atatsetseleka pa mastep abus ikuenda ulendo wa ku mangochi pa katerela 8km away 4m KR through kamuzu bridg,ku Salima.Izi zachitka 4-5pm pasanathe 30min mdipiti wa JB utangodutsa kumene.Dzina,mudzi,zaka,ndi tsiku loika maliro ndikuninkhani mawa Ambuye akatilora.May hz soul RIP.Word,Prayr,Concern&Ques u r welcom.
Posted on: Tue, 15 Oct 2013 18:25:52 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015