Peter Mponda wati bungwe la fam lachita bwino pokonza masewera a - TopicsExpress



          

Peter Mponda wati bungwe la fam lachita bwino pokonza masewera a paubale a team ya Malawi pa 14 august ku Kigali ku Rwanda. Mponda wati masewelowa athandiza kwambiri Malawi kuti ikonzekere bwino Nigeria koma mponda yemwe adanena sabata yatha kuti ndi okonzeka kubwelelanso ku Flames wakana ponena kuti sali okonzeka kukatumikira Flames ku Nigeria kamba kakuti wakhala nthawi yaitali asakudoda chikopa. Iye wati masewera a Nigeria ndi ofunika kwambiri ndi team ikuyenera kupita yokonzeka bwino ndipo sakufunika kupititsa osewera oti sanakonzeke bwino bwino........@Andy (the undisputed)
Posted on: Fri, 02 Aug 2013 06:14:12 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015