WACHITOLA CHITHUMBA CHA NDALAMA MWANA : Katswiri wakale wa Big - TopicsExpress



          

WACHITOLA CHITHUMBA CHA NDALAMA MWANA : Katswiri wakale wa Big Bullets Gabadinho Mhango watola chithumba cha ndalama pamene zadziwika kuti team yake yatsopano, Bloemfontein Celtic idzimulipira 30,000 Rands (pafupi-fupi 1.2 million Kwacha) pa mwezi. Gabadinho Mhango adasaina contract ya chaka chimodzi koma ali ndi mwayi owonjezera zaka zina ziwiri pa contract yake yomwe ilipo panopa.... Zabwino zonse Gabadinho Mhango.........@Andy (the undisputed)
Posted on: Thu, 19 Sep 2013 07:23:56 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015