ZAMATSEME (MATAMA, SHOWBIZZ) ZIMENE AMACHITA ANTHU PA FACEBOOK 1. - TopicsExpress



          

ZAMATSEME (MATAMA, SHOWBIZZ) ZIMENE AMACHITA ANTHU PA FACEBOOK 1. Putting up a status: London is cold, cholinga muwafunse kuti 'mwapita liti?' or kukunyaditsani kuti ali kunja 2.sob sob sob. Status imeneyotu. Then people should be asking 'chavuta ndi chani?' kodi ngati wina wazima osangonena bwanji? 3. My man is out of this world. Thanks for the car dear. Update yokuwuzani kuti achibwenzi awo awagulira vitz eyetu 4. My BB Pin is XYD... Cholinga mudziwe kuti agula blackbail 5. Enjoting beef burger at steers with my man, ati mudziwe kuti akudya ku steers ngakhale akudyazo si burger yi Zina tawonjezerani #Linda
Posted on: Wed, 14 Aug 2013 15:53:27 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015